Oweruza 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Apa nʼkuti anthu atabisalira Samisoni mʼchipinda china. Mkaziyo anamuuza kuti: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Atamva zimenezo, Samisoni anadula zingwe zija ngati mmene ulusi* umadukira ukagwira moto.+ Chinsinsi cha mphamvu zake sichinadziwike.
9 Apa nʼkuti anthu atabisalira Samisoni mʼchipinda china. Mkaziyo anamuuza kuti: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Atamva zimenezo, Samisoni anadula zingwe zija ngati mmene ulusi* umadukira ukagwira moto.+ Chinsinsi cha mphamvu zake sichinadziwike.