Oweruza 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Delila anauza Samisoni kuti: “Wakhala ukundipusitsa pondiuza zabodza.+ Ndiuze zimene angakumange nazo.” Samisoni anayankha kuti: “Umange zingongo 7 zamʼmutu mwanga ndi ulusi wowombera mulitali mwa nsalu.”
13 Kenako Delila anauza Samisoni kuti: “Wakhala ukundipusitsa pondiuza zabodza.+ Ndiuze zimene angakumange nazo.” Samisoni anayankha kuti: “Umange zingongo 7 zamʼmutu mwanga ndi ulusi wowombera mulitali mwa nsalu.”