Oweruza 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Delila anauza Samisoni kuti: “Nʼchifukwa chiyani umanena kuti, ‘Ndimakukonda,’+ chonsecho mtima wako suli pa ine? Wakhala ukundipusitsa katatu konse ndipo sunandiuze chimene chimakuchititsa kuti ukhale ndi mphamvu zambiri.”+
15 Ndiyeno Delila anauza Samisoni kuti: “Nʼchifukwa chiyani umanena kuti, ‘Ndimakukonda,’+ chonsecho mtima wako suli pa ine? Wakhala ukundipusitsa katatu konse ndipo sunandiuze chimene chimakuchititsa kuti ukhale ndi mphamvu zambiri.”+