Oweruza 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa chakuti Delila ankapanikiza Samisoni tsiku lililonse komanso kumuumiriza kuti amuuze, Samisoni anafika potopa nazo kwambiri moti sakanathanso kupirira.+
16 Chifukwa chakuti Delila ankapanikiza Samisoni tsiku lililonse komanso kumuumiriza kuti amuuze, Samisoni anafika potopa nazo kwambiri moti sakanathanso kupirira.+