Oweruza 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Delila ataona kuti Samisoni wamuululira zonse, nthawi yomweyo anatumiza uthenga kwa olamulira a Afilisiti,+ wakuti: “Tsopano bwerani chifukwa wandiululira zonse.” Choncho olamulira a Afilisitiwo anabwera kwa Delila atatenga ndalama zija.
18 Delila ataona kuti Samisoni wamuululira zonse, nthawi yomweyo anatumiza uthenga kwa olamulira a Afilisiti,+ wakuti: “Tsopano bwerani chifukwa wandiululira zonse.” Choncho olamulira a Afilisitiwo anabwera kwa Delila atatenga ndalama zija.