-
Oweruza 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kenako Delila anachititsa kuti Samisoni agone tulo pamiyendo pake, ndipo anaitana munthu wina kuti amʼmete zingongo 7 za mʼmutu mwake. Zitatero Samisoni analibenso mphamvu kwa Delila chifukwa mphamvu zake zinamʼchokera.
-