Oweruza 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Delila anati: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Samisoni atamva zimenezi anadzuka nʼkunena kuti: “Ndipita ngati mmene ndimachitira muja+ ndipo ndipulumuka.” Koma sanadziwe kuti Yehova anali atamusiya.
20 Ndiyeno Delila anati: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Samisoni atamva zimenezi anadzuka nʼkunena kuti: “Ndipita ngati mmene ndimachitira muja+ ndipo ndipulumuka.” Koma sanadziwe kuti Yehova anali atamusiya.