Oweruza 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Afilisiti anamʼgwira ndipo anamuboola maso. Kenako anapita naye ku Gaza nʼkumumanga ndi matcheni awiri akopa,* ndipo iye ankayendetsa mwala wa mphero mʼndende.
21 Choncho Afilisiti anamʼgwira ndipo anamuboola maso. Kenako anapita naye ku Gaza nʼkumumanga ndi matcheni awiri akopa,* ndipo iye ankayendetsa mwala wa mphero mʼndende.