Oweruza 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu ataona Samisoni, anayamba kutamanda mulungu wawo. Iwo ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu, munthu amene wawononga dziko lathu,+ ndiponso kupha anthu ambiri amtundu wathu.”+
24 Anthu ataona Samisoni, anayamba kutamanda mulungu wawo. Iwo ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu, munthu amene wawononga dziko lathu,+ ndiponso kupha anthu ambiri amtundu wathu.”+