-
Oweruza 16:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Chifukwa choti anasangalala kwambiri, anayamba kunena kuti: “Katengeni Samisoni kuti adzatisangalatse.” Choncho anakamutenga kundende kuti adzawasangalatse ndipo anamuimika pakati pa zipilala.
-