-
Oweruza 16:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 (Pa nthawiyi nʼkuti mʼnyumbamo mutadzaza amuna ndi akazi. Olamulira onse a Afilisiti analinso momwemo. Padenga la nyumbayo panali amuna ndi akazi pafupifupi 3,000 amene ankaonerera Samisoni akuwasangalatsa.)
-