Oweruza 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Samisoni+ anafuulira Yehova, kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, chonde ndikumbukireni ndi kundipatsa mphamvu+ kamodzi kokhaka. Inu Mulungu, ndiloleni ndiwabwezere Afilisitiwa chifukwa cha limodzi mwa maso angawa.”+
28 Ndiyeno Samisoni+ anafuulira Yehova, kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, chonde ndikumbukireni ndi kundipatsa mphamvu+ kamodzi kokhaka. Inu Mulungu, ndiloleni ndiwabwezere Afilisitiwa chifukwa cha limodzi mwa maso angawa.”+