Oweruza 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako azichimwene ake ndi anthu onse akubanja la bambo ake, anapita kukatenga mtembo wa Samisoni nʼkudzauika mʼmanda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli. Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+
31 Kenako azichimwene ake ndi anthu onse akubanja la bambo ake, anapita kukatenga mtembo wa Samisoni nʼkudzauika mʼmanda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli. Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+