-
Oweruza 17:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho anabweza ndalama zasiliva zokwana 1,100 zija kwa mayi ake. Koma mayi akewo anati: “Ndalamazi ndizipereka kwa Yehova kuti zikhale zopatulika. Ndikufuna kuti iweyo ugwiritse ntchito ndalamazi kukapangitsa chifaniziro chosema ndiponso chifaniziro chachitsulo.+ Choncho ndikukupatsa ndalamazi.”
-