Oweruza 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mika anali ndi nyumba ya milungu ndipo anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake udindo woti akhale wansembe wake.+
5 Mika anali ndi nyumba ya milungu ndipo anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake udindo woti akhale wansembe wake.+