Oweruza 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Bwanji uzikhala ndi ine ndipo ukhale mlangizi* komanso wansembe wanga? Ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, zovala komanso chakudya.” Atatero Mleviyo analowa mʼnyumba.
10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Bwanji uzikhala ndi ine ndipo ukhale mlangizi* komanso wansembe wanga? Ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, zovala komanso chakudya.” Atatero Mleviyo analowa mʼnyumba.