Oweruza 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atabwerera kwa abale awo ku Zora ndi ku Esitaoli,+ abale awowo anawafunsa kuti: “Mwayendako bwanji?”
8 Atabwerera kwa abale awo ku Zora ndi ku Esitaoli,+ abale awowo anawafunsa kuti: “Mwayendako bwanji?”