Oweruza 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zitatero amuna 600 okhala ndi zida zankhondo, ochokera mʼbanja la Dani, ananyamuka ku Zora ndi ku Esitaoli.+
11 Zitatero amuna 600 okhala ndi zida zankhondo, ochokera mʼbanja la Dani, ananyamuka ku Zora ndi ku Esitaoli.+