Oweruza 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atachoka pamenepo, anakafika kudera lamapiri la Efuraimu ndipo anapita kunyumba ya Mika.+