Oweruza 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna 5 amene anapita kukafufuza malo aja+ anapita kuti akatenge chifaniziro chosema, efodi,+ aterafi*+ ndi chifaniziro chachitsulo.+ (Wansembe uja+ anali ataima pageti ndi amuna 600 okhala ndi zida zankhondowo.)
17 Amuna 5 amene anapita kukafufuza malo aja+ anapita kuti akatenge chifaniziro chosema, efodi,+ aterafi*+ ndi chifaniziro chachitsulo.+ (Wansembe uja+ anali ataima pageti ndi amuna 600 okhala ndi zida zankhondowo.)