Oweruza 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo analowa mʼnyumba ya Mika nʼkutenga chifaniziro chosema, efodi, aterafi* ndi chifaniziro chachitsulo. Atatero wansembeyo anawafunsa kuti: “Mukutani kodi?”
18 Iwo analowa mʼnyumba ya Mika nʼkutenga chifaniziro chosema, efodi, aterafi* ndi chifaniziro chachitsulo. Atatero wansembeyo anawafunsa kuti: “Mukutani kodi?”