-
Oweruza 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Atayenda kamtunda ndithu kuchokera panyumba ya Mika, anthu a mʼnyumba zoyandikana ndi nyumba ya Mika anasonkhana nʼkuyamba kutsatira anthu a fuko la Dani mpaka kuwapeza.
-