-
Oweruza 18:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Iye anayankha kuti: “Mwatenga milungu yanga imene ndinapanga komanso mwatenga wansembe. Nanga ine nditsala ndi chiyani? Ndiye mungandifunse bwanji kuti, ‘Vuto lako nʼchiyani?’”
-