-
Oweruza 18:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Anthu a fuko la Dani anamuuza kuti: “Khala chete! Tisamvenso mawu ako, chifukwa anthu okwiya angakuvulazeni, ndipo mwinanso akhoza kukupha iweyo komanso anthu a mʼnyumba yako.”
-