Oweruza 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu a fuko la Dani atatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe wake, anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu osatekeseka aja.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga nʼkuwotcha mzindawo.
27 Anthu a fuko la Dani atatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe wake, anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu osatekeseka aja.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga nʼkuwotcha mzindawo.