Oweruza 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anthu a fuko la Dani anaimika chifaniziro chosema+ chija. Yonatani+ mwana wa Gerisomu,+ mwana wa Mose, komanso ana ake anakhala ansembe a fuko la Dani mpaka tsiku limene anthu okhala kumeneku anatengedwa kupita ku ukapolo.
30 Kenako anthu a fuko la Dani anaimika chifaniziro chosema+ chija. Yonatani+ mwana wa Gerisomu,+ mwana wa Mose, komanso ana ake anakhala ansembe a fuko la Dani mpaka tsiku limene anthu okhala kumeneku anatengedwa kupita ku ukapolo.