-
Oweruza 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Zitatero, mwamuna wakeyo anapita kukakambirana naye kuti abwerere. Pa ulendowo anali ndi mtumiki wake komanso abulu awiri. Atafika, mkaziyo analowetsa mwamunayo mʼnyumba ya bambo ake ndipo bambowo atamuona anasangalala kwambiri.
-