Oweruza 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mwamunayo sanavomere kuti agonenso. Choncho ananyamuka ndipo anayenda mpaka kukafika pafupi ndi Yebusi yemwenso ndi Yerusalemu.+ Pa ulendowu anali ndi abulu awiri aja, okhala ndi zishalo ndipo analinso ndi mkazi wake komanso mtumiki wake.
10 Koma mwamunayo sanavomere kuti agonenso. Choncho ananyamuka ndipo anayenda mpaka kukafika pafupi ndi Yebusi yemwenso ndi Yerusalemu.+ Pa ulendowu anali ndi abulu awiri aja, okhala ndi zishalo ndipo analinso ndi mkazi wake komanso mtumiki wake.