-
Oweruza 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pamene ankayandikira Yebusi, dzuwa linali litatsala pangʼono kulowa ndipo mtumiki uja anauza mbuye wake kuti: “Bwanji tipite mumzinda wa Ayebusiwu kuti tikagone kumeneko?”
-