Oweruza 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patapita nthawi, bambo wina wachikulire anatulukira madzulowo akuchokera kumunda. Bamboyu kwawo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo pa nthawiyi ankakhala ku Gibeya, koma anthu a mumzindawo anali a fuko la Benjamini.+
16 Patapita nthawi, bambo wina wachikulire anatulukira madzulowo akuchokera kumunda. Bamboyu kwawo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo pa nthawiyi ankakhala ku Gibeya, koma anthu a mumzindawo anali a fuko la Benjamini.+