Oweruza 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tili ndi udzu wokwanira komanso chakudya china cha abulu+ athu ndipo tilinso ndi mkate+ ndi vinyo zokwanira ineyo, mkaziyu komanso mtumiki wathuyu. Chilichonse tili nacho.”
19 Tili ndi udzu wokwanira komanso chakudya china cha abulu+ athu ndipo tilinso ndi mkate+ ndi vinyo zokwanira ineyo, mkaziyu komanso mtumiki wathuyu. Chilichonse tili nacho.”