-
Oweruza 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake ndipo anapatsa abulu akewo chakudya. Kenako anasamba mapazi awo nʼkuyamba kudya ndi kumwa.
-