Oweruza 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu. Amuna oyenda pansi okhala ndi malupanga analipo 400,000.+
2 Kenako, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu. Amuna oyenda pansi okhala ndi malupanga analipo 400,000.+