Oweruza 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu a fuko la Benjamini anamva kuti amuna a Isiraeli apita ku Mizipa. Kenako amuna a Isiraeli anati: “Tafotokozani, kodi zinthu zoipa chonchi zinachitika bwanji?”+
3 Anthu a fuko la Benjamini anamva kuti amuna a Isiraeli apita ku Mizipa. Kenako amuna a Isiraeli anati: “Tafotokozani, kodi zinthu zoipa chonchi zinachitika bwanji?”+