Oweruza 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinatenga thupi la mkazi wanga nʼkuliduladula mapisi ndipo ndinatumiza mapisiwo mʼdera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinachita zimenezi chifukwa zomwe anachitazo nʼzoipa kwambiri komanso nʼzochititsa manyazi mu Isiraeli.
6 Choncho ndinatenga thupi la mkazi wanga nʼkuliduladula mapisi ndipo ndinatumiza mapisiwo mʼdera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinachita zimenezi chifukwa zomwe anachitazo nʼzoipa kwambiri komanso nʼzochititsa manyazi mu Isiraeli.