Oweruza 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero anthu onse ananyamuka mogwirizana,* ndipo anati: “Palibe amene abwerere kutenti yake kapena kunyumba kwake.
8 Zitatero anthu onse ananyamuka mogwirizana,* ndipo anati: “Palibe amene abwerere kutenti yake kapena kunyumba kwake.