-
Oweruza 20:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipo mʼmafuko onse a Isiraeli titengemo amuna 10 pa amuna 100 alionse, amuna 100 pa amuna 1,000 alionse komanso amuna 1,000 pa amuna 10,000 alionse. Amuna amenewa azikatengera asilikali zofunika, kuti apite kukamenyana ndi anthu a ku Gibeya wa ku Benjamini chifukwa cha zinthu zochititsa manyazi zimene achita mu Isiraeli.”
-