-
Oweruza 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Tsiku limenelo anthu a fuko la Benjamini anasonkhanitsa amuna onyamula malupanga okwanira 26,000 kuchokera mʼmizinda yawo, osawerengera amuna 700 a ku Gibeya osankhidwa mwapadera.
-