-
Oweruza 20:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pakati pa asilikali amenewa, panali amuna amanzere 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa amuna amenewa ankatha kuponya mwala nʼkugenda tsitsi limodzi osaphonya.
-