Oweruza 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Aisiraeli anapita ku Beteli kukafunsa kwa Mulungu+ kuti: “Ndani akuyenera kutitsogolera kunkhondo yokamenyana ndi fuko la Benjamini?” Yehova anayankha kuti: “Yuda akutsogolereni.”
18 Ndipo Aisiraeli anapita ku Beteli kukafunsa kwa Mulungu+ kuti: “Ndani akuyenera kutitsogolera kunkhondo yokamenyana ndi fuko la Benjamini?” Yehova anayankha kuti: “Yuda akutsogolereni.”