Oweruza 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero, amuna onse a Isiraeli anapita ku Beteli. Kumeneko analira nʼkukhala pansi pamaso pa Yehova+ ndipo anasala kudya+ mpaka madzulo. Iwo anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+
26 Zitatero, amuna onse a Isiraeli anapita ku Beteli. Kumeneko analira nʼkukhala pansi pamaso pa Yehova+ ndipo anasala kudya+ mpaka madzulo. Iwo anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+