-
Oweruza 20:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Masiku amenewo Pinihasi,+ mwana wa Eliezara, mwana wa Aroni, ndi amene ankatumikira* pafupi ndi likasalo. Choncho amuna a Isiraeli anafunsa kuti: “Kodi tipitenso kukamenyana ndi abale athu a fuko la Benjamini kapena basi tisapitenso?”+ Yehova anayankha kuti: “Pitani, chifukwa mawa ndiwapereka mʼmanja mwanu.”
-