Oweruza 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero Aisiraeli anaika amuna kuti abisale+ kuzungulira mzinda wonse wa Gibeya.