Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Anthu a fuko la Benjamini atapita kukamenyana nawo, Aisiraeliwo anachititsa kuti anthu a fuko la Benjamini atuluke nʼkupita kutali ndi mzindawo.+ Ndiyeno, mofanana ndi mmene zinkachitikira maulendo ena aja, anthu a fuko la Benjaminiwo anayamba kupha ena mwa amuna a Isiraeliwo mʼmisewu ikuluikulu. Msewu wina unali wopita ku Beteli ndipo wina unali wopita ku Gibeya. Iwo anapha amuna 30 a Isiraeli ndipo mitembo yawo inali mbwee.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena