-
Oweruza 20:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panabuka nkhondo yoopsa. Koma anthu a fuko la Benjamini sankadziwa kuti atsala pangʼono kukumana ndi tsoka.
-