Oweruza 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a fuko la Benjamini+ ankaganiza kuti popeza kuti Aisiraeli akuthawa, ndiye kuti akugonja. Koma Aisiraeliwo ankathawa chifukwa ankadalira anzawo amene anabisala pafupi ndi mzinda wa Gibeya+ aja.
36 Anthu a fuko la Benjamini+ ankaganiza kuti popeza kuti Aisiraeli akuthawa, ndiye kuti akugonja. Koma Aisiraeliwo ankathawa chifukwa ankadalira anzawo amene anabisala pafupi ndi mzinda wa Gibeya+ aja.