-
Oweruza 21:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Aisiraeli anayamba kumva chisoni chifukwa cha zimene zinachitikira mchimwene wawo Benjamini. Iwo anati: “Lero fuko limodzi ladulidwa ndi kuchotsedwa mu Isiraeli.
-