Oweruza 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ku Yabesi-giliyadi anapezako atsikana 400, amene anali anamwali oti sanagonepo ndi mwamuna. Atsikanawa anabwera nawo kumsasa ku Silo,+ mʼdziko la Kanani.
12 Ku Yabesi-giliyadi anapezako atsikana 400, amene anali anamwali oti sanagonepo ndi mwamuna. Atsikanawa anabwera nawo kumsasa ku Silo,+ mʼdziko la Kanani.