Oweruza 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthuwo anamva chisoni ndi zimene zinachitikira fuko la Benjamini,+ chifukwa Yehova anachititsa kuti mafuko a Isiraeli agawanike.
15 Anthuwo anamva chisoni ndi zimene zinachitikira fuko la Benjamini,+ chifukwa Yehova anachititsa kuti mafuko a Isiraeli agawanike.