-
Oweruza 21:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiyeno ena anayankha kuti: “Payenera kukhala cholowa kwa anthu a fuko la Benjamini amene apulumuka kuti pasakhale fuko limene lafafanizidwa mu Isiraeli.
-